Achinyamata khumi ndi awiri awathamangitsa ku Israel (Malawi 24)

Achinyamata khumi ndi awiri omwe anayiwala kuti ukayendera n’zengo usati asakhwi afumbura, awathamangitsa m’dziko la Israel kamba kotaya chingamu chifukwa cha mtedza olawa. Sabata latha, a Polisi m’dzikolo anamanga achinyamata okwana makumi anayi ndi mphambu zisanu chifukwa chothawa ntchito zosiyanasiyana zomwe anapitira m’dzikolo ndikupita kukayamba ntchito ku kampani zina m’dziko momwemo.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023