A boma atsutsa mphekesera zomwe zikumveka zoti wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima analetsedwa kutulukira a Malawi amene akhudzidwa ndi mphepo ya namondwe ya Freddy. A Malawi ambiri akhala

Read more