Chipani cha Umodzi chasankha mtsogoleri watsopano (Malawi 24)

Nthumwi ku msonkhano waukulu wa chipani cha Umodzi Party (UP) zasankha mtsogoleri watsopano yemwe akuyembekezeleka kugwira ntchito yawo kwa zaka zisanu.  Pa msonkhano omwe udachitikira ku Robin’s Park Lamulungu mu mzinda wa Blantyre, a Thomas Kaumba asankhidwa kukhala mtsogoleri watsopano wa chipanichi atagonjetsa a Mary Piyasi ndi mavoti 59 kwa 29.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023