Mwana wakhanda wamiyezi yosachepera itatu yemwe mai ake sakudziwika wapezeka atafa mumtsinje wa Likangala mu Mzinda wa Zomba. A Auzious Chimalala omwe amakhala m’mudzi mwa Chilupsa mu Mzinda wa Zomba awuza Malawi24

Read more