Ndife wokonzeka kuchititsa zisankho – MEC (Malawi 24)

Bungwe lowona za zisankho la Malaŵi Electoral Commission (MEC) lanenetsa kuti kuyenda bwino kwa  zisankho zapatatu mu 2025 kudalira kuti anthu amvetse bwino ndondomeko ya kayendetsedwe kazisankhozi. M’modzi mwa makomishonala a bungweli, Dr Anthony Mukumbwa, anena izi lachinayi ku Mzimba pa msonkhano wolimbikitsa mafumu, atsogoleri a mipingo, mabungwe a Civil Society (CSOs) ndi ena onse […] The post Ndife wokonzeka kuchititsa zisankho – MEC appeared first on Malawi 24.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023