Sukulu ya Msiki iwomboledwa ndi ophunzira akale apa Mzuzu University (Malawi 24)

Sukula ya sekondale ya Msiki m’boma la Mzimba ikusimba lokoma potsatira thandizo lokwanira 4.3 miliyoni  lomwe lalandira kuchokera kwa ophunzira akale pa sukulu yaukachenjede ya Mzuzu.  Masiku anayi apitawo,  ophunzira akale pa Mzuzu University anadzidzimutsa sukulu ya Msika ndi thandizo la mabuku olemberamo komanso  ndalama zimene zigwire ntchito ngati sukulu fizi kwa ana khumi ndi […] The post Sukulu ya Msiki iwomboledwa ndi ophunzira akale apa Mzuzu University appeared first on Malawi 24.

More on malawi24.com

 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023