Malawi 24 - Zipani za United Democratic Front (UDF) ndi UTM zadandaula kuti chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chimapereka thumba la ufa lolemera 25 kilogalamu komanso ndalama kwa anthu omwe aponye voti pachisankho chachibwereza pa 26 September chosankha khansala ku Ntiya Ward mu Mzinda wa Zomba zomwe akuti ndizoletsedwa pamalamulo achisankho.

More on malawi24.com

Pin It
 
Crédits

Agence Olloweb : Etude et conduite de projet, prototypage, graphisme, codage de l'environnement graphique - Publinoves communication : Logotype - Orthographe Plus : Rédactionnels - SiteGround : Hébergement - Google : Statistiques, polices de caractères - Développement : HTML5, CSS3, JQUERY, PHP7 - Applications : Adobe® Photoshop®, Adobe® Illustrator®, Panic® Nova® - Année/projet: 2022-2023