Afrique
Vuto la ma pasipoti lizatha? A Zikhale akuti makina alipowo akuchedwa, akupanga mapasipoti 500 okha pa tsiku
Nyasatimes | Nduna yoona za m’dziko a Ken Zikhale Ng’oma yati makina amene akuwagwiritsa ntchito posindikiza ziphaso zoyendera (passports) akugwira ntchitoyo mochedwa kwambiri. Ndunayi yati makinawa akumasindikiza ziphaso zosadutsa 500 patsiku zimene zikuchititsa ntchitoyi kumagwirika mochedwa.
- Catégorie : Nyasa Times